Add parallel Print Page Options

Yesu Mbuye wa Sabata

12 Pa nthawi imeneyo Yesu anadutsa pakati pa minda ya tirigu pa tsiku la Sabata. Ophunzira ake anamva njala nayamba kuthyola ngala za tirigu nʼkumadya. Afarisi ataona zimenezi anati kwa Iye, “Taonani! Ophunzira anu akuchita zosaloledwa pa tsiku la Sabata.”

Iye anayankha kuti, “Kodi simunawerenge zimene anachita Davide pamene iye ndi anzake anamva njala? Analowa mʼNyumba ya Mulungu, ndipo iye ndi anzakewo anadya buledi wopatulika amene sikunali kololedwa kwa iwo kudya koma ansembe okha. Kodi simunawerenge mʼmalamulo kuti pa Sabata ansembe mʼNyumba ya Mulungu amaphwanya lamulo la Sabata komabe sawayesa olakwa? Ine ndikuwuzani kuti wamkulu kuposa Nyumba ya Mulunguyo ali pano. Ngati mukanadziwa zomwe mawu awa atanthauza, ‘Ine ndifuna chifundo osati nsembe,’ inu simukanatsutsa osalakwa. Pakuti Mwana wa Munthu ndiye Mbuye wa Sabata.”

Yesu Achiritsa Munthu Wolumala Dzanja

Atachoka kumeneko anakalowa mʼsunagoge mwawo. 10 Ndipo mʼmenemo munali munthu wolumala dzanja. Pofuna chifukwa chokamunenezera, iwo anamufunsa Yesu kuti, “Kodi nʼkololedwa kuchiritsa munthu tsiku la Sabata?”

11 Iye anawawuza kuti, “Ngati wina wa inu ali ndi nkhosa nigwera mʼdzenje tsiku la Sabata, kodi simudzayigwira ndi kuyitulutsa kunja? 12 Nanga munthu sali oposa nkhosa kwambiri! Chifukwa chake nʼkololedwa kuchita zabwino pa Sabata.”

13 Pamenepo Yesu anati kwa munthuyo, “Wongola dzanja lako.” Iye analiwongola ndipo linakhala monga linalili kale. 14 Koma Afarisi anatuluka kunja ndi kukonza njira yoti amuphere.

Mtumiki Wosankhidwa ndi Mulungu

15 Podziwa zimenezi, Yesu anachoka kumalo amenewo. Ambiri anamutsata Iye ndipo anachiritsira odwala awo onse 16 nawachenjeza kuti asamuwulule kuti yani. 17 Uku kunali kukwaniritsa zimene zinayankhulidwa kudzera mwa mneneri Yesaya kuti,

18 “Taonani mnyamata wanga amene ndinamusankha,
    Wokondedwa wanga, amene moyo wanga ukondwera naye.
Pa Iye ndidzayika Mzimu wanga,
    ndipo Iye adzalalikira chiweruzo kwa akunja.
19 Sadzalimbana, sadzafuwula,
    ngakhale mmodzi sadzamva mawu ake mʼmakwalala.
20 Bango lophwanyika sadzalithyola,
    ndi nyale yofuka sadzayizimitsa,
kufikira Iye adzatumiza chiweruziro chikagonjetse.
21     Ndipo akunja adzakhulupirira dzina lake.”

Mwano wa Afarisi

22 Pomwepo anthu anabwera naye kwa Yesu munthu wogwidwa ndi chiwanda amene anali wosaona ndi wosamva ndipo Yesu anamuchiritsa kotero kuti atatha anayamba kumva ndi kuona. 23 Anthu onse anadabwa ndipo anati, “Kodi uyu ndi kukhala mwana wa Davide?”

24 Koma Afarisi atamva zimenezi, anati, “Uyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebabu mkulu wa ziwandazo.”

25 Yesu anadziwa maganizo awo ndipo anawawuza kuti, “Ufumu uliwonse ukagawanika mwa iwo udzawonongeka ndi mzinda uliwonse kapena banja likagawanika, mwa izo zokha sizidzayima. 26 Ngati Satana atulutsa Satana, iye adzigawa yekha. Nanga ufumu wake ungayime bwanji? 27 Ndipo ngati Ine nditulutsa ziwanda ndi Belezebule, anthu anu amatulutsa ziwandazo ndi chiyani? Potero tsono adzakhala oweruza anu. 28 Koma ngati Ine ndimatulutsa ziwanda ndi Mzimu wa Mulungu, pamenepo ufumu wa Mulungu wafika pa inu.

29 “Kapenanso wina aliyense angathe bwanji kulowa mʼnyumba ya munthu wamphamvu ndi kunyamulamo zinthu zake, sipokhapo atayamba wamanga munthu wa mphamvuyo? Pamenepo iye akhoza kuba mʼnyumbamo.

30 “Iye amene sali ndi Ine atsutsana nane ndipo iye amene sasonkhanitsa pamodzi ndi Ine amamwaza. 31 Ndipo potero Ine ndikuwuzani inu, tchimo lililonse ndi cha mwano chilichonse zidzakhululukidwa kwa anthu koma chamwano cha pa Mzimu Woyera, sichidzakhululukidwa. 32 Aliyense amene anena mawu otsutsana ndi Mwana wa Munthu adzakhululukidwa koma aliyense wonena motsutsana ndi Mzimu Woyera sadzakhululukidwa mu mʼbado uno kapena umene ukubwerawo.

Mtengo ndi Zipatso Zake

33 “Mtengo wabwino umabala zipatso zabwino ndipo mtengo woyipa umabalanso zipatso zoyipa, pajatu mtengo umadziwika ndi zipatso zake. 34 Ana anjoka inu, woyipa inu, mungathe bwanji kuyankhula kanthu kalikonse kabwino? Pakuti pakamwa pamayankhula zosefuka kuchokera mu mtima. 35 Munthu wabwino amatulutsa zinthu zabwino zomwe zili mumtima mwake ndipo munthu woyipa amatulutsanso zinthu zoyipa zomwe zili mwa iye. 36 Ine ndikukuwuzani kuti pa tsiku la chiweruziro munthu adzazengedwa mlandu chifukwa cha mawu aliwonse wopanda pake amene anayankhula. 37 Pakuti ndi mawu anu mudzapezeka osalakwa ndiponso ndi mawu anu mudzapezeka olakwa.”

Chizindikiro cha Yona

38 Pamenepo ena mwa Afarisi ndi aphunzitsi amalamulo anati kwa Iye, “Aphunzitsi, tikufuna tione chizindikiro chodabwitsa kuchokera kwa Inu.”

39 Iye anayankha kuti, “Mʼbado woyipa ndi wachigololo ufunsa za chizindikiro chodabwitsa! Koma ndi chimodzi chomwe sichidzapatsidwa kwa inu kupatula chizindikiro cha mneneri Yona. 40 Pakuti monga Yona anali mʼmimba mwa nsomba yayikulu masiku atatu, usana ndi usiku, momwemonso Mwana wa Munthu adzakhala masiku atatu, usana ndi usiku, mʼkati mwa nthaka. 41 Anthu a ku Ninive adzayimirira pachiweruzo ndi mʼbado uwu ndi kuwutsutsa pakuti iwo analapa Yona atalalikira ndipo tsopano wamkulu kuposa Yona ali pano. 42 Mfumu yayikazi yakummwera idzayimirira pa tsiku lachiweruzo ndi mʼbado uwu ndipo idzawutsutsa pakuti inachokera kumathero a dziko lapansi kudzamva nzeru za Solomoni, ndipo pano pali woposa Solomoni.

Za Mzimu Woyipa

43 “Pamene mzimu woyipa utuluka mwa munthu, umadutsa malo wopanda madzi kufunafuna malo opumulira ndipo suwapeza. 44 Pamenepo umati, ‘Ndidzabwerera ku nyumba yanga komwe ndinatuluka.’ Pamene ufika, upeza mopanda kanthu, mosesedwa ndi mokonzedwa bwino. 45 Kenaka umapita kukatenga mizimu ina isanu ndi iwiri yoyipa kwambiri kuposa uwowo ndipo imapita ndi kukakhala mʼmenemo. Choncho khalidwe lotsiriza la munthu uyu limakhala loyipa kwambiri kuposa loyambalo. Umo ndi mmene zidzakhalire ndi mʼbado oyipawu.”

Amayi ndi Abale Ake a Yesu

46 Pamene Yesu anali kuyankhulabe ndi gulu la anthu, amayi ndi abale ake anayimirira kunja, akufuna kuyankhulana naye. 47 Wina anamuwuza Iye kuti, “Amayi ndi abale anu ayima kunjaku akufuna kuyankhulana nanu.”

48 Iye anayankha kuti, “Amayi anga ndani ndipo abale anga ndi ndani?” 49 Ndipo akuloza ophunzira ake, Iye anati, “Awa ndiwo amayi anga ndi abale anga. 50 Pakuti aliyense amene achita chifuniro cha Atate anga akumwamba ndiye mʼbale wanga, mlongo wanga ndi amayi anga.”

12 At that time Jesus went on the sabbath day through the corn; and his disciples were an hungred, and began to pluck the ears of corn and to eat.

But when the Pharisees saw it, they said unto him, Behold, thy disciples do that which is not lawful to do upon the sabbath day.

But he said unto them, Have ye not read what David did, when he was an hungred, and they that were with him;

How he entered into the house of God, and did eat the shewbread, which was not lawful for him to eat, neither for them which were with him, but only for the priests?

Or have ye not read in the law, how that on the sabbath days the priests in the temple profane the sabbath, and are blameless?

But I say unto you, That in this place is one greater than the temple.

But if ye had known what this meaneth, I will have mercy, and not sacrifice, ye would not have condemned the guiltless.

For the Son of man is Lord even of the sabbath day.

And when he was departed thence, he went into their synagogue:

10 And, behold, there was a man which had his hand withered. And they asked him, saying, Is it lawful to heal on the sabbath days? that they might accuse him.

11 And he said unto them, What man shall there be among you, that shall have one sheep, and if it fall into a pit on the sabbath day, will he not lay hold on it, and lift it out?

12 How much then is a man better than a sheep? Wherefore it is lawful to do well on the sabbath days.

13 Then saith he to the man, Stretch forth thine hand. And he stretched it forth; and it was restored whole, like as the other.

14 Then the Pharisees went out, and held a council against him, how they might destroy him.

15 But when Jesus knew it, he withdrew himself from thence: and great multitudes followed him, and he healed them all;

16 And charged them that they should not make him known:

17 That it might be fulfilled which was spoken by Esaias the prophet, saying,

18 Behold my servant, whom I have chosen; my beloved, in whom my soul is well pleased: I will put my spirit upon him, and he shall shew judgment to the Gentiles.

19 He shall not strive, nor cry; neither shall any man hear his voice in the streets.

20 A bruised reed shall he not break, and smoking flax shall he not quench, till he send forth judgment unto victory.

21 And in his name shall the Gentiles trust.

22 Then was brought unto him one possessed with a devil, blind, and dumb: and he healed him, insomuch that the blind and dumb both spake and saw.

23 And all the people were amazed, and said, Is not this the son of David?

24 But when the Pharisees heard it, they said, This fellow doth not cast out devils, but by Beelzebub the prince of the devils.

25 And Jesus knew their thoughts, and said unto them, Every kingdom divided against itself is brought to desolation; and every city or house divided against itself shall not stand:

26 And if Satan cast out Satan, he is divided against himself; how shall then his kingdom stand?

27 And if I by Beelzebub cast out devils, by whom do your children cast them out? therefore they shall be your judges.

28 But if I cast out devils by the Spirit of God, then the kingdom of God is come unto you.

29 Or else how can one enter into a strong man's house, and spoil his goods, except he first bind the strong man? and then he will spoil his house.

30 He that is not with me is against me; and he that gathereth not with me scattereth abroad.

31 Wherefore I say unto you, All manner of sin and blasphemy shall be forgiven unto men: but the blasphemy against the Holy Ghost shall not be forgiven unto men.

32 And whosoever speaketh a word against the Son of man, it shall be forgiven him: but whosoever speaketh against the Holy Ghost, it shall not be forgiven him, neither in this world, neither in the world to come.

33 Either make the tree good, and his fruit good; or else make the tree corrupt, and his fruit corrupt: for the tree is known by his fruit.

34 O generation of vipers, how can ye, being evil, speak good things? for out of the abundance of the heart the mouth speaketh.

35 A good man out of the good treasure of the heart bringeth forth good things: and an evil man out of the evil treasure bringeth forth evil things.

36 But I say unto you, That every idle word that men shall speak, they shall give account thereof in the day of judgment.

37 For by thy words thou shalt be justified, and by thy words thou shalt be condemned.

38 Then certain of the scribes and of the Pharisees answered, saying, Master, we would see a sign from thee.

39 But he answered and said unto them, An evil and adulterous generation seeketh after a sign; and there shall no sign be given to it, but the sign of the prophet Jonas:

40 For as Jonas was three days and three nights in the whale's belly; so shall the Son of man be three days and three nights in the heart of the earth.

41 The men of Nineveh shall rise in judgment with this generation, and shall condemn it: because they repented at the preaching of Jonas; and, behold, a greater than Jonas is here.

42 The queen of the south shall rise up in the judgment with this generation, and shall condemn it: for she came from the uttermost parts of the earth to hear the wisdom of Solomon; and, behold, a greater than Solomon is here.

43 When the unclean spirit is gone out of a man, he walketh through dry places, seeking rest, and findeth none.

44 Then he saith, I will return into my house from whence I came out; and when he is come, he findeth it empty, swept, and garnished.

45 Then goeth he, and taketh with himself seven other spirits more wicked than himself, and they enter in and dwell there: and the last state of that man is worse than the first. Even so shall it be also unto this wicked generation.

46 While he yet talked to the people, behold, his mother and his brethren stood without, desiring to speak with him.

47 Then one said unto him, Behold, thy mother and thy brethren stand without, desiring to speak with thee.

48 But he answered and said unto him that told him, Who is my mother? and who are my brethren?

49 And he stretched forth his hand toward his disciples, and said, Behold my mother and my brethren!

50 For whosoever shall do the will of my Father which is in heaven, the same is my brother, and sister, and mother.

Jesus Is Lord of the Sabbath(A)

12 At that time (B)Jesus went through the grainfields on the Sabbath. And His disciples were hungry, and began to (C)pluck heads of grain and to eat. And when the Pharisees saw it, they said to Him, “Look, Your disciples are doing what is not lawful to do on the Sabbath!”

But He said to them, “Have you not read (D)what David did when he was hungry, he and those who were with him: how he entered the house of God and ate (E)the showbread which was not lawful for him to eat, nor for those who were with him, (F)but only for the priests? Or have you not read in the (G)law that on the Sabbath the priests in the temple [a]profane the Sabbath, and are blameless? Yet I say to you that in this place there is (H)One greater than the temple. But if you had known what this means, (I)‘I desire mercy and not sacrifice,’ you would not have condemned the guiltless. For the Son of Man is Lord [b]even of the Sabbath.”

Healing on the Sabbath(J)

(K)Now when He had departed from there, He went into their synagogue. 10 And behold, there was a man who had a withered hand. And they asked Him, saying, (L)“Is it lawful to heal on the Sabbath?”—that they might accuse Him.

11 Then He said to them, “What man is there among you who has one sheep, and if it falls into a pit on the Sabbath, will not lay hold of it and lift it out? 12 Of how much more value then is a man than a sheep? Therefore it is lawful to do good on the Sabbath.” 13 Then He said to the man, “Stretch out your hand.” And he stretched it out, and it was restored as whole as the other. 14 Then (M)the Pharisees went out and plotted against Him, how they might destroy Him.

Behold, My Servant

15 But when Jesus knew it, (N)He withdrew from there. (O)And great [c]multitudes followed Him, and He healed them all. 16 Yet He (P)warned them not to make Him known, 17 that it might be fulfilled which was spoken by Isaiah the prophet, saying:

18 “Behold!(Q) My Servant whom I have chosen,
My Beloved (R)in whom My soul is well pleased!
I will put My Spirit upon Him,
And He will declare justice to the Gentiles.
19 He will not quarrel nor cry out,
Nor will anyone hear His voice in the streets.
20 A bruised reed He will not break,
And smoking flax He will not quench,
Till He sends forth justice to victory;
21 And in His name Gentiles will trust.”

A House Divided Cannot Stand(S)

22 (T)Then one was brought to Him who was demon-possessed, blind and mute; and He healed him, so that the [d]blind and mute man both spoke and saw. 23 And all the multitudes were amazed and said, “Could this be the (U)Son of David?”

24 (V)Now when the Pharisees heard it they said, “This fellow does not cast out demons except by [e]Beelzebub, the ruler of the demons.”

25 But Jesus (W)knew their thoughts, and said to them: “Every kingdom divided against itself is brought to desolation, and every city or house divided against itself will not stand. 26 If Satan casts out Satan, he is divided against himself. How then will his kingdom stand? 27 And if I cast out demons by Beelzebub, by whom do your sons cast them out? Therefore they shall be your judges. 28 But if I cast out demons by the Spirit of God, (X)surely the kingdom of God has come upon you. 29 (Y)Or how can one enter a strong man’s house and plunder his goods, unless he first binds the strong man? And then he will plunder his house. 30 He who is not with Me is against Me, and he who does not gather with Me scatters abroad.

The Unpardonable Sin(Z)

31 “Therefore I say to you, (AA)every sin and blasphemy will be forgiven men, (AB)but the blasphemy against the Spirit will not be forgiven men. 32 Anyone who (AC)speaks a word against the Son of Man, (AD)it will be forgiven him; but whoever speaks against the Holy Spirit, it will not be forgiven him, either in this age or in the age to come.

A Tree Known by Its Fruit(AE)

33 “Either make the tree good and (AF)its fruit good, or else make the tree bad and its fruit bad; for a tree is known by its fruit. 34 (AG)Brood[f] of vipers! How can you, being evil, speak good things? (AH)For out of the abundance of the heart the mouth speaks. 35 A good man out of the good treasure [g]of his heart brings forth good things, and an evil man out of the evil treasure brings forth evil things. 36 But I say to you that for every idle word men may speak, they will give account of it in the day of judgment. 37 For by your words you will be justified, and by your words you will be condemned.”

The Scribes and Pharisees Ask for a Sign(AI)

38 (AJ)Then some of the scribes and Pharisees answered, saying, “Teacher, we want to see a sign from You.”

39 But He answered and said to them, “An evil and (AK)adulterous generation seeks after a sign, and no sign will be given to it except the sign of the prophet Jonah. 40 (AL)For as Jonah was three days and three nights in the belly of the great fish, so will the Son of Man be three days and three nights in the heart of the earth. 41 (AM)The men of Nineveh will rise up in the judgment with this generation and (AN)condemn it, (AO)because they repented at the preaching of Jonah; and indeed a greater than Jonah is here. 42 (AP)The queen of the South will rise up in the judgment with this generation and condemn it, for she came from the ends of the earth to hear the wisdom of Solomon; and indeed a greater than Solomon is here.

An Unclean Spirit Returns(AQ)

43 (AR)“When an unclean spirit goes out of a man, (AS)he goes through dry places, seeking rest, and finds none. 44 Then he says, ‘I will return to my house from which I came.’ And when he comes, he finds it empty, swept, and put in order. 45 Then he goes and takes with him seven other spirits more wicked than himself, and they enter and dwell there; (AT)and the last state of that man is worse than the first. So shall it also be with this wicked generation.”

Jesus’ Mother and Brothers Send for Him(AU)

46 While He was still talking to the multitudes, (AV)behold, His mother and (AW)brothers stood outside, seeking to speak with Him. 47 Then one said to Him, “Look, (AX)Your mother and Your brothers are standing outside, seeking to speak with You.”

48 But He answered and said to the one who told Him, “Who is My mother and who are My brothers?” 49 And He stretched out His hand toward His disciples and said, “Here are My mother and My (AY)brothers! 50 For (AZ)whoever does the will of My Father in heaven is My brother and sister and mother.”

Footnotes

  1. Matthew 12:5 desecrate
  2. Matthew 12:8 NU, M omit even
  3. Matthew 12:15 NU brackets multitudes as disputed.
  4. Matthew 12:22 NU omits blind and
  5. Matthew 12:24 NU, M Beelzebul, a Philistine deity
  6. Matthew 12:34 Offspring
  7. Matthew 12:35 NU, M omit of his heart

Jesus Is Lord of the Sabbath

12 At that time (A)Jesus went through the grainfields on the Sabbath. His disciples were hungry, and (B)they began to pluck heads of grain and to eat. But when the Pharisees saw it, they said to him, (C)“Look, your disciples are doing (D)what is not lawful to do on the Sabbath.” He said to them, (E)“Have you not read what David did when he was hungry, and those who were with him: how he entered the house of God and ate (F)the bread of the Presence, which it was not lawful for him to eat nor for those who were with him, but only for the priests? Or have you not read (G)in the Law how on the Sabbath the priests in the temple profane the Sabbath and are guiltless? I tell you, (H)something greater than the temple is here. And if you had known (I)what this means, (J)‘I desire mercy, and not sacrifice,’ you would not have condemned the guiltless. For (K)the Son of Man is lord of the Sabbath.”

A Man with a Withered Hand

He went on from there and (L)entered their synagogue. 10 And a man was there with a withered hand. And they asked him, (M)“Is it lawful to heal on the Sabbath?”—(N)so that they might accuse him. 11 He said to them, “Which one of you who has a sheep, (O)if it falls into a pit on the Sabbath, will not take hold of it and lift it out? 12 (P)Of how much more value is a man than a sheep! So (Q)it is lawful to do good on the Sabbath.” 13 Then he said to the man, “Stretch out your hand.” And (R)the man stretched it out, and it was restored, healthy like the other. 14 But the Pharisees went out and conspired against him, how to destroy him.

God's Chosen Servant

15 Jesus, aware of this, (S)withdrew from there. And (T)many followed him, and he healed them all 16 and (U)ordered them not to make him known. 17 (V)This was to fulfill what was spoken by the prophet Isaiah:

18 (W)“Behold, my (X)servant whom I have chosen,
    my beloved with whom my soul is well pleased.
(Y)I will put my Spirit upon him,
    and he will proclaim justice to the Gentiles.
19 He will not quarrel or cry aloud,
    nor will anyone hear his voice in the streets;
20 a bruised reed he will not break,
    and a smoldering wick he will not quench,
until he brings justice to victory;
21     (Z)and in his name the Gentiles will hope.”

Blasphemy Against the Holy Spirit

22 (AA)Then a demon-oppressed man who was blind and mute was brought to him, and he healed him, so that the man spoke and saw. 23 (AB)And all the people were amazed, and said, (AC)“Can this be the Son of David?” 24 But when the Pharisees heard it, they said, (AD)“It is only by Beelzebul, the prince of demons, that this man casts out demons.” 25 (AE)Knowing their thoughts, (AF)he said to them, “Every kingdom divided against itself is laid waste, and no city or house divided against itself will stand. 26 And if Satan casts out Satan, he is divided against himself. How then will his kingdom stand? 27 And if I cast out demons by Beelzebul, (AG)by whom do (AH)your sons cast them out? Therefore they will be your judges. 28 But if it is (AI)by the Spirit of God that I cast out demons, then (AJ)the kingdom of God has come upon you. 29 Or (AK)how can someone enter a strong man's house and plunder his goods, unless he first binds the strong man? Then indeed (AL)he may plunder his house. 30 (AM)Whoever is not with me is against me, and whoever does not gather with me scatters. 31 (AN)Therefore I tell you, every sin and blasphemy will be forgiven people, but (AO)the blasphemy against the Spirit will not be forgiven. 32 And whoever speaks a word (AP)against the Son of Man (AQ)will be forgiven, but (AR)whoever speaks against the Holy Spirit will not be forgiven, either in (AS)this age or in the age to come.

A Tree Is Known by Its Fruit

33 (AT)“Either make the tree good and its fruit good, or make the tree bad and its fruit bad, (AU)for the tree is known by its fruit. 34 (AV)You brood of vipers! How can you speak good, (AW)when you are evil? (AX)For out of the abundance of the heart the mouth speaks. 35 (AY)The good person out of his good treasure brings forth good, and the evil person out of his evil treasure brings forth evil. 36 I tell you, (AZ)on the day of judgment (BA)people will give account for (BB)every careless word they speak, 37 for (BC)by your words you will be justified, and by your words you will be condemned.”

The Sign of Jonah

38 Then some of the scribes and Pharisees answered him, saying, “Teacher, (BD)we wish to see a sign from you.” 39 But he answered them, (BE)“An evil and (BF)adulterous generation seeks for a sign, but no sign will be given to it except the sign of the prophet Jonah. 40 For (BG)just as Jonah was three days and three nights in the belly of the great fish, (BH)so will the Son of Man be three days and three nights in the heart of the earth. 41 (BI)The men of Nineveh will rise up at the judgment with this generation and (BJ)condemn it, for (BK)they repented at the preaching of Jonah, and behold, (BL)something greater than Jonah is here. 42 (BM)The queen of the South will rise up at the judgment with this generation and condemn it, for she came from the ends of the earth to hear the wisdom of Solomon, and behold, (BN)something greater than Solomon is here.

Return of an Unclean Spirit

43 “When (BO)the unclean spirit has gone out of a person, it passes through (BP)waterless places seeking rest, but finds none. 44 Then it says, ‘I will return to my house from which I came.’ And when it comes, it finds the house empty, swept, and put in order. 45 Then it goes and brings with it seven other spirits more evil than itself, and they enter and dwell there, and (BQ)the last state of that person is worse than the first. So also will it be with this (BR)evil generation.”

Jesus' Mother and Brothers

46 While he was still speaking to the people, behold, (BS)his mother and his (BT)brothers[a] stood outside, asking to speak to him.[b] 48 But he replied to the man who told him, “Who is my mother, and who are my brothers?” 49 And stretching out his hand toward his disciples, he said, “Here are my mother and my brothers! 50 For (BU)whoever (BV)does the will of my Father in heaven is my brother and sister and mother.”

Footnotes

  1. Matthew 12:46 Or brothers and sisters; also verses 48, 49
  2. Matthew 12:46 Some manuscripts insert verse 47: Someone told him, “Your mother and your brothers are standing outside, asking to speak to you”