Add parallel Print Page Options

Yesu Achiritsa Munthu pa Sabata

Patapita nthawi Yesu anakwera kupita ku Yerusalemu ku phwando la Ayuda. Ndipo ku Yerusalemuko pafupi ndi chipata cha Nkhosa kuli dziwe limene mʼChihebri limatchedwa Betisaida ndipo ndi lozunguliridwa ndi makumbi asanu. Mʼmenemo munkagonamo gulu lalikulu la anthu odwala, osaona, olumala ndi ofa ziwalo. Pakuti nthawi zina mngelo wa Ambuye ankatsikira mʼdziwemo nʼkuvundula madziwo. Woyamba kulowamo madzi atavundulidwa, ankachira ngakhale akhale ndi nthenda yanji. Mmodzi wa amene anali pamenepo anali atadwala zaka 38. Yesu atamuona ali chigonere, nadziwa kuti anakhala chotero kwa nthawi yayitali, anamufunsa iye kuti, “Kodi ukufuna kuchira?”

Wodwalayo anayankha kuti, “Ambuye, ndilibe wina aliyense woti angandithandize kulowa mʼdziwe pamene madzi avundulidwa. Pamene ndikuyesera kuti ndilowemo, wina amalowamo ine ndisanalowemo.”

Ndipo Yesu anati kwa iye, “Imirira! Nyamula mphasa yako yamba kuyenda.” Nthawi yomweyo munthuyo anachiritsidwa. Iye ananyamula mphasa yake nayamba kuyenda.

Tsiku limene izi zinachitika linali la Sabata. 10 Ndipo Ayuda anati kwa munthu amene anachiritsidwayo, “Lero ndi la Sabata; lamulo silikulola iwe kunyamula mphasa yako.”

11 Koma iye anayankha kuti, “Munthu amene wandichiritsa anati kwa ine, ‘Nyamula mphasa yako yamba kuyenda.’ ”

12 Pamenepo anamufunsa iye kuti, “Kodi munthu ameneyo ndani amene wakuwuza kuti, ‘Nyamula mphasa yako ndipo yenda?’ ”

13 Munthu amene anachiritsidwayo sanadziwe kuti anali ndani, pakuti Yesu anangolowera mʼgulu la anthu ndi kupita.

14 Patapita nthawi Yesu anamupeza ku Nyumba ya Mulungu ndipo anati kwa iye, “Taona uli bwino tsopano. Usakachimwenso kuti choyipa choposa ichi chingakugwere.” 15 Munthu uja anachoka ndi kukawawuza Ayuda kuti anali Yesu amene anamuchiritsa iye.

Yesu Adziwulula kuti ndi Mwana wa Mulungu

16 Ndipo popeza Yesu amachita zinthu izi tsiku la Sabata, Ayuda anayamba kumulondalonda. 17 Yesu anawawuza kuti, “Atate anga amagwira ntchito nthawi zonse mpaka lero lino, ndipo Inenso ndili pa ntchito.” 18 Chifukwa cha ichi Ayuda anawirikiza kufuna kumupha; osati chifukwa chakuswa Sabata kokha komanso chifukwa ankanena kuti Mulungu ndi Atate ake, nadziyesa Iye wofanana ndi Mulungu.

19 Yesu anawapatsa yankho ili: “Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti Mwana sangathe kuchita kanthu pa Iye yekha. Iye amachita zokhazo zimene amaona Atate ake akuchita, chifukwa chilichonse chimene Atate amachita Mwana amachitanso. 20 Pakuti Atate amakonda Mwana, amamuonetsa zonse zimene Iwo amachita. Inde, Atate adzamuonetsa zinthu zazikulu kuposa zimenezi ndipo mudzadabwa. 21 Pakuti monga Atate amaukitsa akufa nawapatsa moyo, momwemonso Mwana amapereka moyo kwa amene Iye akufuna. 22 Komanso, Atate saweruza aliyense koma wapereka kwa Mwana ulamuliro woweruzawo, 23 kuti aliyense alemekeze Mwanayo monga momwe amalemekezera Atate. Munthu amene salemekeza Mwana salemekezanso Atate amene anamutuma Mwanayo.

24 “Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti aliyense amene amamva mawu anga ndi kukhulupirira Iye amene ananditumiza Ine, ali ndi moyo wosatha ndipo sadzaweruzidwa. Iye wachoka mu imfa ndipo walowa mʼmoyo. 25 Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti nthawi ikubwera ndipo yafika kale tsopano, pamene akufa adzamva mawu a Mwana wa Mulungu ndipo iwo amene amva adzakhala ndi moyo. 26 Pakuti monga Atate ali gwero la moyo, momwemonso anapereka mphamvu zopereka moyo mwa Mwana. 27 Ndipo wamupatsa Iye ulamuliro woweruza chifukwa ndi Mwana wa Munthu.

28 “Musadabwe ndi zimenezi. Pakuti nthawi ikubwera pamene onse amene ali mʼmanda adzamva mawu ake 29 ndi kutuluka. Iwo amene anachita zabwino adzauka ndi kupita ku moyo wosatha ndipo amene anachita zoyipa adzauka ndi kupita ku chilango chamuyaya. 30 Pakuti sindingathe kuchita kena kalikonse pa ndekha. Ine ndimaweruza molingana ndi zomwe Mulungu wandiwuza ndipo kuweruza kwanga ndi kolungama. Ine sindifuna kudzikondweretsa ndekha koma Iye amene anandituma.

Maumboni Onena za Yesu

31 “Ngati ndidzichitira umboni ndekha, umboni wanga si woona. 32 Alipo wina amene amandichitira umboni wabwino. Ine ndikudziwa kuti umboni wake wonena za Ine ndi woona.

33 “Inu munatumiza amithenga kwa Yohane ndipo iye anachitira umboni choona. 34 Sikuti Ine ndikudalira umboni wa munthu; koma ndikunena zimenezi kuti mupulumutsidwe. 35 Yohane anali ngati nyale imene imayaka ndi kuwala, ndipo inu kwa kanthawi munasankha kusangalala ndi kuwala kwakeko.

36 “Koma Ine ndili ndi umboni woposa uja wa Yohane. Pakuti ntchito imene Atate andipatsa kuti ndiyikwaniritse ndi imene ndikugwira, ndipo ikundichitira umboni kuti Atate andituma Ine. 37 Ndipo Atate amene anandituma Ine, Iye mwini wandichitira umboni. Inu simunamvepo mawu ake kapena kuona maonekedwe ake, 38 kapena mawu ake kukhala mwa inu, pakuti simukhulupirira Iye amene anamutuma. 39 Inu mumasanthula malemba chifukwa mumaganiza kuti mʼmalembamo muli moyo wosatha. Awa ndi malemba amene akundichitira umboni. 40 Koma inu mukukana kubwera kwa Ine kuti mukhale ndi moyo.

41 “Ine sindilandira ulemu kuchokera kwa anthu 42 koma Ine ndikukudziwani. Ndikudziwa kuti mʼmitima mwanu mulibe chikondi cha Mulungu. 43 Ine ndabwera mʼdzina la Atate anga, ndipo inu simukundirandira Ine; koma wina wake akabwera mʼdzina la iye mwini, inu mudzamulandira. 44 Kodi inu mudzakhulupirira bwanji ngati mumapatsana ulemu wina ndi mnzake, ndipo simufuna kulandira ulemu kuchokera kwa Mulungu yekhayo?

45 “Koma inu musaganize kuti Ine ndidzakunenezani kwa Atate. Wokunenezani ndi Mose, amene inu mwayikapo chiyembekezo chanu. 46 Ngati mukanakhulupirira Mose, mukanakhulupiriranso Ine, pakuti iye analemba za Ine. 47 Koma ngati simukhulupirira zimene iye analemba, mudzakhulupirira bwanji zimene Ine ndikunena?”

A Man Healed at the Pool of Bethesda

After (A)this there was a feast of the Jews, and Jesus (B)went up to Jerusalem. Now there is in Jerusalem (C)by the Sheep Gate a pool, which is called in Hebrew, [a]Bethesda, having five porches. In these lay a great multitude of sick people, blind, lame, [b]paralyzed, [c]waiting for the moving of the water. For an angel went down at a certain time into the pool and stirred up the water; then whoever stepped in first, after the stirring of the water, was made well of whatever disease he had. Now a certain man was there who had an infirmity thirty-eight years. When Jesus saw him lying there, and knew that he already had been in that condition a long time, He said to him, “Do you want to be made well?”

The sick man answered Him, “Sir, I have no man to put me into the pool when the water is stirred up; but while I am coming, another steps down before me.”

Jesus said to him, (D)“Rise, take up your bed and walk.” And immediately the man was made well, took up his bed, and walked.

And (E)that day was the Sabbath. 10 The Jews therefore said to him who was cured, “It is the Sabbath; (F)it is not lawful for you to carry your bed.”

11 He answered them, “He who made me well said to me, ‘Take up your bed and walk.’

12 Then they asked him, “Who is the Man who said to you, ‘Take up your bed and walk’?” 13 But the one who was (G)healed did not know who it was, for Jesus had withdrawn, a multitude being in that place. 14 Afterward Jesus found him in the temple, and said to him, “See, you have been made well. (H)Sin no more, lest a worse thing come upon you.”

15 The man departed and told the Jews that it was Jesus who had made him well.

Honor the Father and the Son

16 For this reason the Jews (I)persecuted Jesus, [d]and sought to kill Him, because He had done these things on the Sabbath. 17 But Jesus answered them, (J)“My Father has been working until now, and I have been working.”

18 Therefore the Jews (K)sought all the more to kill Him, because He not only broke the Sabbath, but also said that God was His Father, (L)making Himself equal with God. 19 Then Jesus answered and said to them, “Most assuredly, I say to you, (M)the Son can do nothing of Himself, but what He sees the Father do; for whatever He does, the Son also does in like manner. 20 For (N)the Father loves the Son, and (O)shows Him all things that He Himself does; and He will show Him greater works than these, that you may marvel. 21 For as the Father raises the dead and gives life to them, (P)even so the Son gives life to whom He will. 22 For the Father judges no one, but (Q)has committed all judgment to the Son, 23 that all should honor the Son just as they honor the Father. (R)He who does not honor the Son does not honor the Father who sent Him.

Life and Judgment Are Through the Son

24 “Most assuredly, I say to you, (S)he who hears My word and believes in Him who sent Me has everlasting life, and shall not come into judgment, (T)but has passed from death into life. 25 Most assuredly, I say to you, the hour is coming, and now is, when (U)the dead will hear the voice of the Son of God; and those who hear will live. 26 For (V)as the Father has life in Himself, so He has granted the Son to have (W)life in Himself, 27 and (X)has given Him authority to execute judgment also, (Y)because He is the Son of Man. 28 Do not marvel at this; for the hour is coming in which all who are in the graves will (Z)hear His voice 29 (AA)and come forth—(AB)those who have done good, to the resurrection of life, and those who have done evil, to the resurrection of condemnation. 30 (AC)I can of Myself do nothing. As I hear, I judge; and My judgment is righteous, because (AD)I do not seek My own will but the will of the Father who sent Me.

The Fourfold Witness

31 (AE)“If I bear witness of Myself, My witness is not [e]true. 32 (AF)There is another who bears witness of Me, and I know that the witness which He witnesses of Me is true. 33 You have sent to John, (AG)and he has borne witness to the truth. 34 Yet I do not receive testimony from man, but I say these things that you may be saved. 35 He was the burning and (AH)shining lamp, and (AI)you were willing for a time to rejoice in his light. 36 But (AJ)I have a greater witness than John’s; for (AK)the works which the Father has given Me to finish—the very (AL)works that I do—bear witness of Me, that the Father has sent Me. 37 And the Father Himself, who sent Me, (AM)has testified of Me. You have neither heard His voice at any time, (AN)nor seen His form. 38 But you do not have His word abiding in you, because whom He sent, Him you do not believe. 39 (AO)You search the Scriptures, for in them you think you have eternal life; and (AP)these are they which testify of Me. 40 (AQ)But you are not willing to come to Me that you may have life.

41 (AR)“I do not receive honor from men. 42 But I know you, that you do not have the love of God in you. 43 I have come in My Father’s name, and you do not receive Me; if another comes in his own name, him you will receive. 44 (AS)How can you believe, who receive honor from one another, and do not seek (AT)the honor that comes from the only God? 45 Do not think that I shall accuse you to the Father; (AU)there is one who accuses you—Moses, in whom you trust. 46 For if you believed Moses, you would believe Me; (AV)for he wrote about Me. 47 But if you (AW)do not believe his writings, how will you believe My words?”

Footnotes

  1. John 5:2 NU Bethzatha
  2. John 5:3 withered
  3. John 5:3 NU omits the rest of v. 3 and all of v. 4.
  4. John 5:16 NU omits and sought to kill Him
  5. John 5:31 valid as testimony

The Healing at the Pool on the Sabbath

After this there was a (A)feast of the Jews, and Jesus went up to Jerusalem.

Now there is in Jerusalem by (B)the Sheep Gate a pool, in Aramaic[a] called Bethesda,[b] which has five roofed colonnades. In these lay a multitude of invalids—blind, lame, and (C)paralyzed.[c] One man was there who had been an invalid for thirty-eight years. When Jesus saw him lying there and knew that he had already been there a long time, he said to him, “Do you want to be healed?” The sick man answered him, “Sir, I have no one to put me into the pool when the water is stirred up, and while I am going another steps down before me.” Jesus said to him, (D)“Get up, take up your bed, and walk.” (E)And at once the man was healed, and he took up his bed and walked.

(F)Now that day was the Sabbath. 10 So the Jews[d] said to the man who had been healed, “It is the Sabbath, and (G)it is not lawful for you to take up your bed.” 11 But he answered them, “The man who healed me, that man said to me, ‘Take up your bed, and walk.’ 12 They asked him, “Who is the man who said to you, ‘Take up your bed and walk’?” 13 Now the man who had been healed did not know who it was, for (H)Jesus had withdrawn, as there was a crowd in the place. 14 Afterward Jesus found him in the temple and said to him, “See, you are well! (I)Sin no more, (J)that nothing worse may happen to you.” 15 The man went away and told the Jews that it was Jesus who had healed him. 16 And this was why the Jews (K)were persecuting Jesus, (L)because he was doing these things on the Sabbath. 17 But Jesus answered them, “My Father is working until now, and I am working.”

Jesus Is Equal with God

18 This was why the Jews (M)were seeking all the more to kill him, (N)because not only was he (O)breaking the Sabbath, but he was even calling God (P)his own Father, (Q)making himself equal with God.

The Authority of the Son

19 So Jesus said to them, “Truly, truly, I say to you, (R)the Son (S)can do nothing of his own accord, but only what he sees the Father doing. For whatever the Father[e] does, that the Son does likewise. 20 For (T)the Father loves the Son and shows him all that he himself is doing. And (U)greater works than these will he show him, so that (V)you may marvel. 21 For as the Father (W)raises the dead and (X)gives them life, so (Y)also the Son gives life (Z)to whom he will. 22 (AA)For the Father judges no one, but (AB)has given all judgment to the Son, 23 that all may honor the Son, just as they (AC)honor the Father. (AD)Whoever does not honor the Son does not honor the Father who sent him. 24 Truly, truly, I say to you, (AE)whoever hears my word and (AF)believes him who sent me has eternal life. He (AG)does not come into judgment, but (AH)has passed from death to life.

25 “Truly, truly, I say to you, (AI)an hour is coming, and is now here, when (AJ)the dead will hear (AK)the voice of the Son of God, and those who hear (AL)will live. 26 (AM)For as the Father has life in himself, (AN)so he has granted the Son also to have life in himself. 27 And he (AO)has given him authority to execute judgment, because he is the Son of Man. 28 Do not marvel at this, for (AP)an hour is coming when (AQ)all who are in the tombs will hear his voice 29 and come out, (AR)those who have done good to the resurrection of life, and those who have done evil to the resurrection of judgment.

Witnesses to Jesus

30 (AS)“I can do nothing on my own. As I hear, I judge, and (AT)my judgment is just, because (AU)I seek not my own will (AV)but the will of him who sent me. 31 (AW)If I alone bear witness about myself, my testimony is not true. 32 There is (AX)another who bears witness about me, and (AY)I know that the testimony that he bears about me is true. 33 (AZ)You sent to John, and he has borne witness to the truth. 34 Not that (BA)the testimony that I receive is from man, but I say these things so that you may be saved. 35 He was a burning and (BB)shining lamp, and (BC)you were willing to rejoice for a while in his light. 36 But (BD)the testimony that I have is greater than that of John. For (BE)the works that the Father has given me (BF)to accomplish, the very works that I am doing, (BG)bear witness about me that (BH)the Father has sent me. 37 And the Father who sent me (BI)has himself borne witness about me. His voice you have never heard, (BJ)his form you have never seen, 38 and (BK)you do not have his word abiding in you, for you do not believe the one whom he has sent. 39 (BL)You search the Scriptures because you think that in them you have eternal life; and (BM)it is they that bear witness about me, 40 yet (BN)you refuse to come to me that you may have life. 41 (BO)I do not receive glory from people. 42 But (BP)I know that you do not have (BQ)the love of God within you. 43 I have come (BR)in my Father's name, and (BS)you do not receive me. (BT)If another comes in his own name, you will receive him. 44 How can you believe, when you receive glory from one another and (BU)do not seek the glory that comes from (BV)the only God? 45 Do not think that I will accuse you to the Father. There is one who accuses you: Moses, (BW)on whom you have set your hope. 46 For if you believed Moses, you would believe me; for (BX)he wrote of me. 47 But (BY)if you do not believe his writings, how will you believe my words?”

Footnotes

  1. John 5:2 Or Hebrew
  2. John 5:2 Some manuscripts Bethsaida
  3. John 5:3 Some manuscripts insert, wholly or in part, waiting for the moving of the water; for an angel of the Lord went down at certain seasons into the pool, and stirred the water: whoever stepped in first after the stirring of the water was healed of whatever disease he had
  4. John 5:10 The Greek word Ioudaioi refers specifically here to Jewish religious leaders, and others under their influence, who opposed Jesus in that time; also verses 15, 16, 18
  5. John 5:19 Greek he

Curación de un paralítico

Después de esto, se celebraba[a] una fiesta[b] de los judíos, y Jesús subió a Jerusalén(A). Hay en Jerusalén, junto a la puerta de las Ovejas(B), un estanque que en hebreo[c](C) se llama Betesda[d] que tiene cinco pórticos. En estos estaba en el suelo una multitud de enfermos, ciegos, cojos y paralíticos [e]que esperaban el movimiento del agua; porque un ángel del Señor descendía de vez en cuando al estanque y agitaba el agua; y el primero que descendía al estanque después del movimiento del agua, quedaba curado de cualquier enfermedad que tuviera.

Estaba allí un hombre que hacía treinta y ocho años que estaba enfermo[f]. Cuando Jesús lo vio acostado allí y supo que ya llevaba mucho tiempo en aquella condición, le dijo*: «¿Quieres ser sano?». El enfermo le respondió: «Señor, no tengo a nadie que me meta en el estanque cuando el agua es agitada(D); y mientras yo llego, otro baja antes que yo». Jesús le dijo*: «Levántate, toma tu camilla(E)y anda». Al instante el hombre quedó sano, y tomó su camilla y comenzó a andar.

Jesús censurado por sanar en el día de reposo

Pero aquel día era día de reposo(F).

10 Por eso los judíos(G) decían al que había sido sanado: «Es día de reposo, y no te es permitido cargar tu camilla(H)». 11 Pero él les respondió: «El mismo que me sanó, me dijo: “Toma tu camilla y anda”». 12 Le preguntaron: «¿Quién es el hombre que te dijo: “Toma tu camilla y anda”?».

13 Pero el que había sido sanado no sabía quién era, porque Jesús, sin que se dieran cuenta, se había apartado de la multitud que estaba en aquel lugar. 14 Después de esto Jesús lo halló* en el templo y le dijo: «Mira, has sido sanado; no peques más(I), para que no te suceda algo peor(J)».

15 El hombre se fue, y dijo a los judíos(K) que Jesús era el que lo había sanado. 16 A causa de esto los judíos(L) perseguían a Jesús, porque hacía estas cosas en el día de reposo. 17 Pero Jesús les respondió: «Hasta ahora Mi Padre trabaja, y Yo también trabajo». 18 Entonces, por esta causa, los judíos(M) aún más procuraban matar a Jesús, porque no solo violaba el día de reposo(N), sino que también llamaba a Dios Su propio Padre, haciéndose igual a Dios(O).

Unanimidad del Padre y del Hijo

19 Por eso Jesús les decía: «En verdad les digo que el Hijo no puede hacer nada por Su cuenta(P), sino lo que ve hacer al Padre; porque todo lo que hace el Padre[g], eso también hace el Hijo de igual manera. 20 Pues el Padre ama al Hijo(Q), y le muestra todo lo que Él mismo hace; y obras mayores que estas(R)le mostrará, para que ustedes se queden asombrados. 21 Porque así como el Padre levanta a los muertos y les da vida(S), asimismo el Hijo también da vida(T)a los que Él quiere. 22 Porque ni aun el Padre juzga a nadie, sino que todo juicio se lo ha confiado[h]al Hijo(U), 23 para que todos honren al Hijo así como honran al Padre. El que no honra al Hijo, no honra al Padre que lo envió(V).

24 »En verdad les digo: el que oye Mi palabra y cree al que me envió, tiene vida eterna(W) y no viene a condenación[i](X) , sino que ha pasado de muerte a vida(Y) . 25 En verdad les digo que viene la hora, y ahora es(Z), cuando los muertos(AA)oirán la voz del Hijo de Dios, y los que oigan(AB)vivirán. 26 Porque como el Padre tiene vida en Él mismo, así también le dio al Hijo el tener vida en Él mismo(AC); 27 y le dio autoridad para ejecutar juicio(AD), porque Él es el Hijo del Hombre.

28 »No se queden asombrados de esto, porque viene la hora(AE) en que todos los que están en los sepulcros(AF) oirán Su voz, 29 y saldrán: los que hicieron lo bueno, a resurrección de vida, y los que practicaron lo malo, a resurrección de juicio(AG).

Testimonio del Padre y de las obras de Jesús

30 »Yo no puedo hacer nada por iniciativa Mía(AH) ; como oigo, juzgo, y Mi juicio es justo(AI) porque no busco Mi voluntad, sino la voluntad del que me envió(AJ) .

31 »Si Yo solo doy testimonio de Mí mismo(AK) , Mi testimonio no es verdadero[j] . 32 Otro es el que da testimonio de Mí(AL), y Yo sé que el testimonio que da de Mí es verdadero.

33 »Ustedes han enviado a preguntar a Juan, y él ha dado testimonio(AM) de la verdad. 34 Pero el testimonio que Yo recibo no es de hombre(AN); pero digo esto para que ustedes sean salvos. 35 Él era la lámpara que ardía y alumbraba(AO), y ustedes estaban dispuestos a regocijarse por un tiempo en su luz(AP).

36 »Pero el testimonio que Yo tengo es mayor que el de Juan; porque las obras que el Padre me ha dado para llevar a cabo(AQ) , las mismas obras que Yo hago, dan testimonio de Mí(AR) , de que el Padre me ha enviado(AS) . 37 El Padre que me envió, Él ha dado testimonio de Mí(AT). Pero ustedes no han oído jamás Su voz ni han visto Su apariencia. 38 Y Su palabra no la tienen morando en ustedes(AU), porque no creen en Aquel que Él envió(AV). 39 Ustedes examinan[k]las Escrituras porque piensan tener en ellas la vida eterna(AW). ¡Y son ellas las que dan testimonio de Mí(AX)! 40 Pero ustedes no quieren venir a Mí para que tengan esa vida.

41 »Yo no recibo gloria de los hombres(AY) ; 42 pero a ustedes ya los conozco, que no tienen el amor de Dios. 43 Yo he venido en nombre de Mi Padre y ustedes no me reciben; si otro viene en su propio nombre(AZ), a ese recibirán. 44 ¿Cómo pueden creer, cuando reciben gloria los unos de los otros(BA), y no buscan la gloria que viene del Dios único(BB)?

45 »No piensen que Yo los acusaré delante del Padre; el que los acusa es Moisés(BC) , en quien ustedes han puesto su esperanza. 46 Porque si creyeran a Moisés, me creerían a Mí, porque de Mí escribió él(BD). 47 Pero si no creen sus escritos(BE), ¿cómo creerán Mis palabras?».

Footnotes

  1. 5:1 Lit. había.
  2. 5:1 Algunos mss. dicen: la fiesta; i.e. la Pascua.
  3. 5:2 I.e. en arameo judaico.
  4. 5:2 Otros mss. dicen: Betsaida, o Betzata.
  5. 5:3 Los mss. más antiguos no incluyen el resto del vers. 3 y todo el vers. 4.
  6. 5:5 Lit. con su enfermedad.
  7. 5:19 Lit. aquel.
  8. 5:22 Lit. dado.
  9. 5:24 Lit. a juicio.
  10. 5:31 I.e. admisible como prueba legal.
  11. 5:39 O Examinen.