18 (A)‘The Lord is slow to anger and abounding in steadfast love, forgiving iniquity and transgression, but he will by no means clear the guilty, (B)visiting the iniquity of the fathers on the children, to the third and the fourth generation.’

Read full chapter

18 ‘Yehova sakwiya msanga, ndipo ndi wodzaza ndi chikondi chosasinthika, wokhululukira tchimo ndi kuwukira. Koma Iye sadzaleka kulanga ochimwa. Iyeyo amalanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo kufikira mʼbado wachitatu ndi wachinayi.’

Read full chapter