Font Size
2 Akorinto 3:8-10
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
2 Akorinto 3:8-10
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
8 kodi nanga utumiki wa Mzimu sudzaposa apa? 9 Ngati utumiki umene umatsutsa anthu unali ndi ulemerero, nanga koposa kotani ulemerero wa utumiki wobweretsa chilungamo! 10 Pakuti zimene zinali ndi ulemerero, tsopano zilibenso ulemerero pofananitsa ndi ulemerero wopambanawo.
Read full chapter
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero (CCL)
The Word of God in Contemporary Chichewa Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc.® Used by permission of Biblica, Inc.® All rights reserved worldwide. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc.® Kugwiritsa ntchito mwachilolezo. Umwini ndi otetezedwa pa dziko lonse.