1 Akorinto 11
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
11 Tsatirani chitsanzo changa, monga inenso nditsatira chitsanzo cha Khristu.
Makhalidwe Oyenera pa Mapemphero
2 Ndikukuyamikani chifukwa chondikumbukira pa zonse ndiponso posunga ziphunzitso monga ndinakuphunzitsirani. 3 Tsopano ndikufuna muzindikire kuti Khristu ndiye mutu wa munthu aliyense, ndipo mwamuna ndiye mutu wamkazi, ndipo mutu wa Khristu ndi Mulungu. 4 Mwamuna aliyense wopemphera kapena kunenera ataphimba mutu wake akunyoza mutu wakewo. 5 Ndipo mkazi aliyense wopemphera kapena kunenera asanaphimbe mutu wake sakulemekeza mutu wakewo. Kuli chimodzimodzi kumeta mutu wake. 6 Ngati mkazi saphimba kumutu kwake, ndiye kuti amete tsitsi lake. Ngati nʼchamanyazi kwa mkazi kungoyepula kapena kumeta mpala, ndiye kuti aphimbe kumutu kwake.
7 Mwamuna sayenera kuphimba kumutu popeza ndi chifaniziro ndi ulemerero wa Mulungu; pamene mkazi ndi ulemerero wa mwamuna. 8 Pakuti mwamuna sachokera kwa mkazi, koma mkazi kwa mwamuna. 9 Ndipo mwamuna sanalengedwe chifukwa cha mkazi, koma mkazi analengedwera mwamuna. 10 Pa chifukwa ichi, ndiponso pa chifukwa cha angelo, mkazi akuyenera kukhala ndi chizindikiro cha ulamuliro wake. 11 Komabe mwa Ambuye, mkazi amadalira mwamuna ndipo mwamuna amadalira mkazi. 12 Pakuti monga mkazi anachokera kwa mwamuna, momwemonso mwamuna anabadwa mwa mkazi. Koma zonse zichokera kwa Mulungu.
13 Dziweruzeni. Kodi nʼchabwino kuti mkazi apemphere kwa Mulungu wopanda chophimba kumutu? 14 Kodi chikhalidwe chathu sichitiphunzitsa kuti nʼchamanyazi kuti mwamuna akhale ndi tsitsi lalitali, 15 koma mkazi akakhala ndi tsitsi lalitali ndi ulemerero wake? Pakuti mkazi anapatsidwa tsitsi lalitali monga chophimba kumutu. 16 Ngati wina akufuna kutsutsapo pa zimenezi, ife ndiponso mipingo ya Mulungu tilibe machitidwe ena apadera koma ndi omwewa.
Mgonero wa Ambuye
17 Koma popereka malangizo awa sindikufuna kukuyamikirani popeza mʼmisonkhano yanu mumachita zoyipa kuposa zabwino. 18 Choyamba, ndikumva kuti mukasonkhana mu mpingo mumasankhana ndipo ndikukhulupirira kuti zimenezi kwinaku nʼzoona. 19 Nʼzosakayikitsa kuti pali kugawikana pakati panu kuti adziwike amene ndi ovomerezeka ndi Mulungu. 20 Tsono, mukasonkhana pamodzi, chimene mumadya si Mgonero wa Ambuye. 21 Pakuti mukamadya, aliyense amangodzidyera zomwe anakonza. Wina amakhala ndi njala pamene wina amaledzera. 22 Kodi mulibe nyumba zanu kumene mungamadyere ndi kumwa? Kapena mumapeputsa mpingo wa Mulungu ndi kuchititsa manyazi amene alibe kalikonse? Ndikunena chiyani kwa inu? Moti ndikuyamikireni pa zimenezi? Ayi, pa zinthu izi sindingakuyamikireni.
23 Pakuti zimene ndinalandira kwa Ambuye ndi zomwe ndinakupatsani. Ambuye Yesu, usiku umene anaperekedwa uja, anatenga buledi. 24 Atayamika ndi kumunyema ananena kuti, “Ili ndi thupi langa lomwe laperekedwa kwa inu; muzichita zimenezi pokumbukira Ine.” 25 Chimodzimodzi, atatha kudya, anatenga chikho, nati, “Chikho ichi ndi pangano latsopano la magazi anga; imwani nthawi zonse pokumbukira Ine.” 26 Pakuti nthawi zonse pamene mudya bulediyu ndikumwa chikhochi, mukulalikira imfa ya Ambuye mpaka Iye adzabweranso.
27 Chifukwa chake, aliyense amene adya buledi kapena kumwa chikho cha Ambuye mʼnjira yosayenera adzachimwira thupi ndi magazi a Ambuye. 28 Munthu adzisanthule yekha asanadye buledi kapena kumwa chikhochi. 29 Popeza aliyense amene adya kapena kumwa mosazindikira thupi la Ambuye, amadya ndi kumwa chiweruzo chake chomwe. 30 Nʼchifukwa chake pakati panu ambiri mwa inu ndi ofowoka ndi odwala, ndipo ambirinso agona tulo. 31 Koma tikanadziyesa tokha sitikaweruzidwanso. 32 Pamene tiweruzidwa ndi Ambuye, ndiye kuti akukonza khalidwe lathu kupewa kuti tingatsutsidwe pamodzi ndi anthu osakhulupirira.
33 Ndiye tsono abale anga, pamene musonkhana pa chakudya, mudikirirane. 34 Ngati wina ali ndi njala, adye ku nyumba kwake kuti pamene musonkhana pamodzi zisafike poti muweruzidwe nazo.
Ndipo ndikabwera ndidzakupatsani malangizo ena owonjezera.
1 Corinthiens 11
La Bible du Semeur
11 Suivez donc mon exemple, comme moi, de mon côté, je suis celui de Christ.
La vie dans la communauté
L’homme et la femme dans l’Eglise
2 Je vous félicite de vous souvenir de moi en toute occasion et de maintenir fidèlement les traditions que je vous ai transmises.
3 Je voudrais cependant attirer votre attention sur un point : Christ est le chef[a] de tout homme, l’homme est le chef de la femme, le chef de Christ, c’est Dieu. 4 Si donc un homme prie ou prophétise la tête couverte, il outrage son chef. 5 Mais si une femme prie ou prophétise la tête non couverte, elle outrage son chef à elle : c’est comme si elle était rasée[b]. 6 Si donc une femme ne se couvre pas la tête, pourquoi, alors, ne se fait-elle pas aussi tondre les cheveux ? Mais s’il est honteux pour une femme d’être tondue ou rasée, qu’elle se couvre donc la tête.
7 L’homme ne doit pas avoir la tête couverte, puisqu’il est l’image de Dieu et reflète sa gloire. La femme, elle, est la gloire de l’homme. 8 En effet, l’homme n’a pas été tiré de la femme, mais la femme de l’homme[c], 9 et l’homme n’a pas été créé à cause de la femme, mais la femme à cause de l’homme. 10 Voilà pourquoi la femme doit porter sur la tête un signe d’autorité[d], à cause des anges. 11 Toutefois, dans l’ordre établi par le Seigneur, la femme n’existe pas sans l’homme, et l’homme n’existe pas sans la femme, 12 car si la femme a été tirée de l’homme, celui-ci, à son tour, naît de la femme et, finalement, tous deux doivent leur vie à Dieu.
13 Jugez vous-mêmes de cela : est-il convenable pour une femme de prier Dieu la tête découverte ? 14 Ne paraît-il pas naturel à tout le monde que c’est une indignité pour un homme de porter des cheveux longs 15 mais qu’une longue chevelure fait honneur à la femme ? Car la chevelure lui a été donnée pour lui servir de voile.
16 Si quelqu’un s’obstine à contester, nous lui répondons que ce qu’il propose n’est ni notre pratique ni celle des Eglises de Dieu.
Le repas du Seigneur
17 Puisque j’en suis aux directives, il me faut mentionner un point pour lequel je ne saurais vous féliciter. C’est que vos réunions, au lieu de contribuer à votre progrès, vous font devenir pires.
18 Tout d’abord j’entends dire que lorsque vous tenez une réunion, il y a parmi vous des divisions. – J’incline à croire qu’il y a une part de vérité dans ce qu’on raconte. 19 Sans doute faut-il qu’il y ait chez vous des divisions, pour que les chrétiens qui ont fait leurs preuves soient clairement reconnus au milieu de vous !
20 Ainsi, lorsque vous vous réunissez, on ne peut vraiment plus appeler cela « prendre le repas du Seigneur », 21 car, à peine êtes-vous à table, que chacun s’empresse de manger ses propres provisions[e], et l’on voit des gens manquer de nourriture pendant que d’autres s’enivrent.
22 S’il ne s’agit que de manger et de boire, n’avez-vous pas vos maisons pour le faire ? Ou bien traitez-vous avec mépris l’Eglise de Dieu et avez-vous l’intention d’humilier les membres pauvres de votre assemblée ?
Que puis-je vous dire ? Vais-je vous féliciter ? Certainement pas. 23 Car voici la tradition que j’ai reçue du Seigneur, et que je vous ai transmise : le Seigneur Jésus, dans la nuit où il fut livré pour être mis à mort, prit du pain[f], 24 et, après avoir prononcé la prière de reconnaissance, il le rompit en disant : « Ceci est mon corps : il est pour vous ; faites ceci en souvenir de moi. » 25 De même, après le repas, il prit la coupe et dit : « Cette coupe est la nouvelle alliance scellée de mon sang ; faites ceci, toutes les fois que vous en boirez, en souvenir de moi. » 26 Donc, chaque fois que vous mangez de ce pain et que vous buvez de cette coupe, vous annoncez la mort du Seigneur, et ceci jusqu’à son retour.
27 C’est pourquoi quiconque mangerait le pain ou boirait de la coupe du Seigneur d’une manière indigne se rendrait coupable envers le corps et le sang du Seigneur. 28 Que chacun donc s’examine sérieusement lui-même et qu’alors il mange de ce pain et boive de cette coupe. 29 Car celui qui mange et boit sans discerner ce qu’est le corps[g] se condamne lui-même en mangeant et en buvant ainsi. 30 C’est pour cette raison qu’il y a parmi vous tant de malades et d’infirmes, et qu’un certain nombre sont morts. 31 Si nous discernions ce que nous sommes, nous ne tomberions pas sous le jugement. 32 Mais les jugements du Seigneur ont pour but de nous corriger afin que nous ne soyons pas condamnés avec le reste du monde.
33 Ainsi donc, frères et sœurs, lorsque vous vous réunissez pour le repas en commun, attendez-vous les uns les autres. 34 Si quelqu’un a particulièrement faim, qu’il mange d’abord chez lui afin que vos réunions n’attirent pas sur vous le jugement de Dieu. Quant aux autres points, je les réglerai lors de mon passage chez vous.
Footnotes
- 11.3 Dans tout ce passage, Paul utilise un mot grec qui signifie à la fois tête et chef.
- 11.5 Selon les normes sociales romaines, en vigueur à Corinthe, les femmes mariées devaient avoir la tête couverte lorsqu’elles se présentaient en public. Cette tenue les protégeait contre les avances masculines. Qu’une femme se présente en public la tête non couverte était considéré comme un rejet de son statut matrimonial. En revanche, on rasait la tête des femmes reconnues coupables d’adultère.
- 11.8 Voir Gn 1.26-27 ; 2.18-23.
- 11.10 Selon les uns cette « autorité » serait celle de la femme, selon les autres il s’agirait de l’autorité de son mari (cf. v. 3-5).
- 11.21 Dans les agapes (repas fraternels) au cours desquelles on célébrait la cène, on apportait des provisions que l’on mettait en commun. A Corinthe, chacun mangeait ce qu’il avait apporté.
- 11.23 Voir Mt 26.26ss ; Mc 14.22-25 ; Lc 22.15-20.
- 11.29 Certains manuscrits précisent : le corps du Seigneur.
1 Corinthians 11
New International Version
11 1 Follow my example,(A) as I follow the example of Christ.(B)
On Covering the Head in Worship
2 I praise you(C) for remembering me in everything(D) and for holding to the traditions just as I passed them on to you.(E) 3 But I want you to realize that the head of every man is Christ,(F) and the head of the woman is man,[a](G) and the head of Christ is God.(H) 4 Every man who prays or prophesies(I) with his head covered dishonors his head. 5 But every woman who prays or prophesies(J) with her head uncovered dishonors her head—it is the same as having her head shaved.(K) 6 For if a woman does not cover her head, she might as well have her hair cut off; but if it is a disgrace for a woman to have her hair cut off or her head shaved, then she should cover her head.
7 A man ought not to cover his head,[b] since he is the image(L) and glory of God; but woman is the glory of man. 8 For man did not come from woman, but woman from man;(M) 9 neither was man created for woman, but woman for man.(N) 10 It is for this reason that a woman ought to have authority over her own[c] head, because of the angels. 11 Nevertheless, in the Lord woman is not independent of man, nor is man independent of woman. 12 For as woman came from man, so also man is born of woman. But everything comes from God.(O)
13 Judge for yourselves: Is it proper for a woman to pray to God with her head uncovered? 14 Does not the very nature of things teach you that if a man has long hair, it is a disgrace to him, 15 but that if a woman has long hair, it is her glory? For long hair is given to her as a covering. 16 If anyone wants to be contentious about this, we have no other practice—nor do the churches of God.(P)
Correcting an Abuse of the Lord’s Supper(Q)
17 In the following directives I have no praise for you,(R) for your meetings do more harm than good. 18 In the first place, I hear that when you come together as a church, there are divisions(S) among you, and to some extent I believe it. 19 No doubt there have to be differences among you to show which of you have God’s approval.(T) 20 So then, when you come together, it is not the Lord’s Supper you eat, 21 for when you are eating, some of you go ahead with your own private suppers.(U) As a result, one person remains hungry and another gets drunk. 22 Don’t you have homes to eat and drink in? Or do you despise the church of God(V) by humiliating those who have nothing?(W) What shall I say to you? Shall I praise you?(X) Certainly not in this matter!
23 For I received from the Lord(Y) what I also passed on to you:(Z) The Lord Jesus, on the night he was betrayed, took bread, 24 and when he had given thanks, he broke it and said, “This is my body,(AA) which is for you; do this in remembrance of me.” 25 In the same way, after supper he took the cup, saying, “This cup is the new covenant(AB) in my blood;(AC) do this, whenever you drink it, in remembrance of me.” 26 For whenever you eat this bread and drink this cup, you proclaim the Lord’s death until he comes.(AD)
27 So then, whoever eats the bread or drinks the cup of the Lord in an unworthy manner will be guilty of sinning against the body and blood of the Lord.(AE) 28 Everyone ought to examine themselves(AF) before they eat of the bread and drink from the cup. 29 For those who eat and drink without discerning the body of Christ eat and drink judgment on themselves. 30 That is why many among you are weak and sick, and a number of you have fallen asleep.(AG) 31 But if we were more discerning with regard to ourselves, we would not come under such judgment.(AH) 32 Nevertheless, when we are judged in this way by the Lord, we are being disciplined(AI) so that we will not be finally condemned with the world.(AJ)
33 So then, my brothers and sisters, when you gather to eat, you should all eat together. 34 Anyone who is hungry(AK) should eat something at home,(AL) so that when you meet together it may not result in judgment.
And when I come(AM) I will give further directions.
Footnotes
- 1 Corinthians 11:3 Or of the wife is her husband
- 1 Corinthians 11:7 Or 4 Every man who prays or prophesies with long hair dishonors his head. 5 But every woman who prays or prophesies with no covering of hair dishonors her head—she is just like one of the “shorn women.” 6 If a woman has no covering, let her be for now with short hair; but since it is a disgrace for a woman to have her hair shorn or shaved, she should grow it again. 7 A man ought not to have long hair
- 1 Corinthians 11:10 Or have a sign of authority on her
1 Corinthians 11
New King James Version
Worship and the Lord’s Supper
11 Imitate(A) me, just as I also imitate Christ.
Head Coverings
2 Now I praise you, brethren, that you remember me in all things and keep the traditions just as I delivered them to you. 3 But I want you to know that (B)the head of every man is Christ, (C)the head of woman is man, and (D)the head of Christ is God. 4 Every man praying or (E)prophesying, having his head covered, dishonors his head. 5 But every woman who prays or prophesies with her head uncovered dishonors her head, for that is one and the same as if her head were (F)shaved. 6 For if a woman is not covered, let her also be shorn. But if it is (G)shameful for a woman to be shorn or shaved, let her be covered. 7 For a man indeed ought not to cover his head, since (H)he is the image and glory of God; but woman is the glory of man. 8 For man is not from woman, but woman (I)from man. 9 Nor was man created for the woman, but woman (J)for the man. 10 For this reason the woman ought to have a symbol of authority on her head, because of the angels. 11 Nevertheless, (K)neither is man independent of woman, nor woman independent of man, in the Lord. 12 For as woman came from man, even so man also comes through woman; but all things are from God.
13 Judge among yourselves. Is it proper for a woman to pray to God with her head uncovered? 14 Does not even nature itself teach you that if a man has long hair, it is a dishonor to him? 15 But if a woman has long hair, it is a glory to her; for her hair is given [a]to her for a covering. 16 But (L)if anyone seems to be contentious, we have no such custom, (M)nor do the churches of God.
Conduct at the Lord’s Supper
17 Now in giving these instructions I do not praise you, since you come together not for the better but for the worse. 18 For first of all, when you come together as a church, (N)I hear that there are divisions among you, and in part I believe it. 19 For (O)there must also be factions among you, (P)that those who are approved may be [b]recognized among you. 20 Therefore when you come together in one place, it is not to eat the Lord’s Supper. 21 For in eating, each one takes his own supper ahead of others; and one is hungry and (Q)another is drunk. 22 What! Do you not have houses to eat and drink in? Or do you despise (R)the church of God and (S)shame [c]those who have nothing? What shall I say to you? Shall I praise you in this? I do not praise you.
Institution of the Lord’s Supper(T)
23 For (U)I received from the Lord that which I also delivered to you: (V)that the Lord Jesus on the same night in which He was betrayed took bread; 24 and when He had given thanks, He broke it and said, [d]“Take, eat; this is My body which is [e]broken for you; do this in remembrance of Me.” 25 In the same manner He also took the cup after supper, saying, “This cup is the new covenant in My blood. This do, as often as you drink it, in remembrance of Me.”
26 For as often as you eat this bread and drink this cup, you proclaim the Lord’s death (W)till He comes.
Examine Yourself
27 Therefore whoever eats (X)this bread or drinks this cup of the Lord in an unworthy manner will be guilty of the body and [f]blood of the Lord. 28 But (Y)let a man examine himself, and so let him eat of the bread and drink of the cup. 29 For he who eats and drinks [g]in an unworthy manner eats and drinks judgment to himself, not discerning the [h]Lord’s body. 30 For this reason many are weak and sick among you, and many [i]sleep. 31 For (Z)if we would judge ourselves, we would not be judged. 32 But when we are judged, (AA)we are chastened by the Lord, that we may not be condemned with the world.
33 Therefore, my brethren, when you (AB)come together to eat, wait for one another. 34 But if anyone is hungry, let him eat at home, lest you come together for judgment. And the rest I will set in order when I come.
Footnotes
- 1 Corinthians 11:15 M omits to her
- 1 Corinthians 11:19 Lit. manifest, evident
- 1 Corinthians 11:22 The poor
- 1 Corinthians 11:24 NU omits Take, eat
- 1 Corinthians 11:24 NU omits broken
- 1 Corinthians 11:27 NU, M the blood
- 1 Corinthians 11:29 NU omits in an unworthy manner
- 1 Corinthians 11:29 NU omits Lord’s
- 1 Corinthians 11:30 Are dead
The Word of God in Contemporary Chichewa Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc.® Used by permission of Biblica, Inc.® All rights reserved worldwide. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc.® Kugwiritsa ntchito mwachilolezo. Umwini ndi otetezedwa pa dziko lonse.
La Bible Du Semeur (The Bible of the Sower) Copyright © 1992, 1999 by Biblica, Inc.®
Used by permission. All rights reserved worldwide.
Holy Bible, New International Version®, NIV® Copyright ©1973, 1978, 1984, 2011 by Biblica, Inc.® Used by permission. All rights reserved worldwide.
NIV Reverse Interlinear Bible: English to Hebrew and English to Greek. Copyright © 2019 by Zondervan.
Scripture taken from the New King James Version®. Copyright © 1982 by Thomas Nelson. Used by permission. All rights reserved.

