Add parallel Print Page Options

12 院子的西面,也要有帷幔,寬二十二公尺。帷幔的柱子十根,插座十個。 13 院子的東面,要有二十二公尺寬。 14 門一面的帷幔要六公尺六公寸,帷幔的柱子三根,插座三個。

Read full chapter

12 “Mbali yakumadzulo ya bwalolo ikhale yotalika mamita 23 ndipo ikhale ndi nsalu yotchinga, nsichi khumi ndi matsinde khumi. 13 Mbali yakummawa, kotulukira dzuwa, kutalika kwa bwalo kukhale mamita 23. 14 Mbali imodzi yachipata kukhale nsalu yotchinga yotalika mamita asanu ndi awiri, mizati itatu ndi matsinde atatu.

Read full chapter